Numeri 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amenewa ndiwo anali ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,600.+
41 Amenewa ndiwo anali ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,600.+