Yoswa 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye ataona kuti asilikali omwe anabisala+ aja alanda mzindawo, ndiponso utsi ukufuka mumzindawo, anatembenukira amuna a ku Ai n’kuyamba kuwapha.
21 Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye ataona kuti asilikali omwe anabisala+ aja alanda mzindawo, ndiponso utsi ukufuka mumzindawo, anatembenukira amuna a ku Ai n’kuyamba kuwapha.