Yoswa 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kum’mwera kwatsala dziko lonse la Akanani. Patsalanso mzinda wa Asidoni+ wotchedwa Meara, mpaka kukafika ku Afeki kumalire a Aamori, Oweruza 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Fuko la Aseri+ silinapitikitse anthu okhala mumzinda wa Ako ndi anthu okhala m’mizinda ya Sidoni,+ Alabu, Akizibu,+ Heliba, Afiki+ ndi Rehobu.+
4 Kum’mwera kwatsala dziko lonse la Akanani. Patsalanso mzinda wa Asidoni+ wotchedwa Meara, mpaka kukafika ku Afeki kumalire a Aamori,
31 Fuko la Aseri+ silinapitikitse anthu okhala mumzinda wa Ako ndi anthu okhala m’mizinda ya Sidoni,+ Alabu, Akizibu,+ Heliba, Afiki+ ndi Rehobu.+