Genesis 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo mtumikiyo anatenga ngamila 10 pa ngamila za mbuye wake, n’kutenganso zabwino za mtundu uliwonse kwa mbuye wake zoti akazigwiritse ntchito.+ Kenako ananyamuka ulendo wopita ku Mesopotamiya, kumzinda wa Nahori.
10 Pamenepo mtumikiyo anatenga ngamila 10 pa ngamila za mbuye wake, n’kutenganso zabwino za mtundu uliwonse kwa mbuye wake zoti akazigwiritse ntchito.+ Kenako ananyamuka ulendo wopita ku Mesopotamiya, kumzinda wa Nahori.