Oweruza 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawi imeneyo Debora mneneri wamkazi,+ mkazi wa Lapidoti, anali kuweruza Isiraeli.