-
Oweruza 4:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pa nthawiyi, Baraki anatulukira akusakasaka Sisera. Pamenepo Yaeli anapita kukamuchingamira, ndipo anamuuza kuti: “Tabwerani ndikuonetseni munthu amene mukum’funafunayo.” Iye anam’tsatira, ndipo anangoona Sisera ali thasa pansi wakufa, chikhomo chili m’mutu mwake pafupi ndi khutu.
-