Oweruza 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa,+ anaphimba chigwa chonse chifukwa cha kuchuluka kwawo ngati dzombe.+ Ngamila zawo+ zinali zosawerengeka, zochuluka ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.
12 Tsopano Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kum’mawa,+ anaphimba chigwa chonse chifukwa cha kuchuluka kwawo ngati dzombe.+ Ngamila zawo+ zinali zosawerengeka, zochuluka ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.