Oweruza 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Manowa anatenga kamwana ka mbuzi ndi nsembe yambewu n’kuzipereka nsembe kwa Yehova pathanthwe.+ Ndipo Mulungu anali kuchita zodabwitsa, Manowa ndi mkazi wake akuonerera.
19 Pamenepo Manowa anatenga kamwana ka mbuzi ndi nsembe yambewu n’kuzipereka nsembe kwa Yehova pathanthwe.+ Ndipo Mulungu anali kuchita zodabwitsa, Manowa ndi mkazi wake akuonerera.