Oweruza 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamene lawi la moto linali kukwera m’mwamba kuchokera paguwalo, mngelo wa Yehova nayenso anakwera kumwamba m’lawi la moto wa paguwa lansembelo, Manowa ndi mkazi wake akuonerera.+ Nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
20 Pamene lawi la moto linali kukwera m’mwamba kuchokera paguwalo, mngelo wa Yehova nayenso anakwera kumwamba m’lawi la moto wa paguwa lansembelo, Manowa ndi mkazi wake akuonerera.+ Nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+