Genesis 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako, Yakobo ananyamuka n’kupitiriza ulendo wake wopita Kum’mawa.+ Oweruza 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.
3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.