Oweruza 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Debora anauza Baraki kuti: “Nyamuka, pakuti lero ndi tsiku limene Yehova adzapereka Sisera m’manja mwako. Yehova akuyendatu patsogolo pako.”+ Ndipo Baraki anatsikadi m’phiri la Tabori, amuna 10,000 akum’tsatira.
14 Kenako Debora anauza Baraki kuti: “Nyamuka, pakuti lero ndi tsiku limene Yehova adzapereka Sisera m’manja mwako. Yehova akuyendatu patsogolo pako.”+ Ndipo Baraki anatsikadi m’phiri la Tabori, amuna 10,000 akum’tsatira.