1 Samueli 17:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Kenako Davide anatenga mutu+ wa Mfilisiti uja ndi kupita nawo ku Yerusalemu, ndipo zida za Mfilisiti uja anaziika muhema wake.+
54 Kenako Davide anatenga mutu+ wa Mfilisiti uja ndi kupita nawo ku Yerusalemu, ndipo zida za Mfilisiti uja anaziika muhema wake.+