Genesis 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa linali litatuluka pamene Yakobo anali kuchoka pa Penueli, koma anali kuyenda chotsimphina.+ Oweruza 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anapitiriza ulendo wake kuchoka kumeneko n’kupita ku Penueli.+ Atafika ku Penueli, anawapemphanso chimodzimodzi, koma amuna a kumeneko anamuyankha mofanana ndi mmene amuna a ku Sukoti anamuyankhira. 1 Mafumu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yerobowamu anamanga mzinda wa Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, n’kuyamba kukhala kumeneko. Kenako anachoka kumeneko n’kupita kukamanga mzinda wa Penueli.+
8 Choncho anapitiriza ulendo wake kuchoka kumeneko n’kupita ku Penueli.+ Atafika ku Penueli, anawapemphanso chimodzimodzi, koma amuna a kumeneko anamuyankha mofanana ndi mmene amuna a ku Sukoti anamuyankhira.
25 Yerobowamu anamanga mzinda wa Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, n’kuyamba kukhala kumeneko. Kenako anachoka kumeneko n’kupita kukamanga mzinda wa Penueli.+