Genesis 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Labani anamuuza kuti: “Ndithu, iwe ndiwe fupa langa ndi mnofu wanga.”+ Choncho anakhala naye mwezi wathunthu. 1 Mbiri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+
14 Ndiyeno Labani anamuuza kuti: “Ndithu, iwe ndiwe fupa langa ndi mnofu wanga.”+ Choncho anakhala naye mwezi wathunthu.
11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+