Hoseya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.
6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.