Yoweli 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu zilombo zakutchire musachite mantha,+ pakuti malo odyetserako ziweto a m’chipululu adzamera msipu wobiriwira.+ Mitengo nayonso idzabereka zipatso.+ Mtengo wa mkuyu ndi mtengo wa mpesa udzatulutsa zipatso zake zonse.+
22 Inu zilombo zakutchire musachite mantha,+ pakuti malo odyetserako ziweto a m’chipululu adzamera msipu wobiriwira.+ Mitengo nayonso idzabereka zipatso.+ Mtengo wa mkuyu ndi mtengo wa mpesa udzatulutsa zipatso zake zonse.+