1 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’
10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’