Oweruza 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anthu ndi akalonga a Giliyadi anayamba kufunsana kuti: “Ndani atitsogolere kukamenyana ndi ana a Amoni?+ Ameneyo akhale mtsogoleri wa anthu onse okhala m’Giliyadi.”+
18 Ndiyeno anthu ndi akalonga a Giliyadi anayamba kufunsana kuti: “Ndani atitsogolere kukamenyana ndi ana a Amoni?+ Ameneyo akhale mtsogoleri wa anthu onse okhala m’Giliyadi.”+