Numeri 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Aisiraeli anatuma amithenga kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Aamori kukanena kuti: Deuteronomo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kenako, ndinatumiza amithenga a mawu amtendere+ kuchokera m’chipululu cha Kademoti,+ kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, kuti, Yoswa 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anawapatsanso mizinda yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori imene inali kulamulira ku Hesiboni, mpaka kumalire ndi ana a Amoni.+
26 “Kenako, ndinatumiza amithenga a mawu amtendere+ kuchokera m’chipululu cha Kademoti,+ kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, kuti,
10 Anawapatsanso mizinda yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori imene inali kulamulira ku Hesiboni, mpaka kumalire ndi ana a Amoni.+