Ezekieli 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘“Unali kuchita malonda ndi Yuda komanso dziko la Isiraeli. Unapereka zinthu zimene unasunga posinthanitsa+ ndi tirigu+ wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu.+
17 “‘“Unali kuchita malonda ndi Yuda komanso dziko la Isiraeli. Unapereka zinthu zimene unasunga posinthanitsa+ ndi tirigu+ wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu.+