-
Oweruza 15:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Pamenepo anthu a ku Yuda anati: “N’chifukwa chiyani mwabwera kudzatiukira?” Poyankha, iwo anati: “Tabwera kudzamanga Samisoni, kuti tim’chitire zimene iye watichitira.”
-