1 Samueli 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Nahasi Muamoni ananena kuti: “Ndidzachita nanu pangano pokhapokha nditaboola diso+ la kudzanja lamanja la aliyense wa inu, kuti chikhale chinthu chotonzetsa Aisiraeli onse.”+ 2 Mafumu 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+
2 Kenako Nahasi Muamoni ananena kuti: “Ndidzachita nanu pangano pokhapokha nditaboola diso+ la kudzanja lamanja la aliyense wa inu, kuti chikhale chinthu chotonzetsa Aisiraeli onse.”+
7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+