1 Mafumu 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe Yehosafati anauza mfumu ya Isiraeli kuti: “Choyamba, umve kaye mawu a Yehova.”+