Deuteronomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu. Salimo 81:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikanagonjetsa adani awo mosavuta,+Ndipo ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+
4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu.