Yoswa 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inuyo mwaona zonse zimene Yehova Mulungu wanu anachitira mitundu yonse chifukwa cha inu.+ Yehova Mulungu wanu ndiye anali kukumenyerani nkhondo.+ Yoswa 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aisiraeli anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse a Yoswa, ndi masiku onse a akulu amene anapitiriza kukhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira,+ omwe ankadziwa ntchito zonse zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+
3 Inuyo mwaona zonse zimene Yehova Mulungu wanu anachitira mitundu yonse chifukwa cha inu.+ Yehova Mulungu wanu ndiye anali kukumenyerani nkhondo.+
31 Aisiraeli anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse a Yoswa, ndi masiku onse a akulu amene anapitiriza kukhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira,+ omwe ankadziwa ntchito zonse zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+