Yeremiya 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Kukubwera Hanameli mwana wa Salumu m’bale wa bambo ako, kudzakuuza kuti: “Ugule munda wanga wa ku Anatoti+ chifukwa iweyo ndi amene uli ndi ufulu wogula mundawo.”’”+
7 ‘Kukubwera Hanameli mwana wa Salumu m’bale wa bambo ako, kudzakuuza kuti: “Ugule munda wanga wa ku Anatoti+ chifukwa iweyo ndi amene uli ndi ufulu wogula mundawo.”’”+