Yoswa 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pambuyo pake, mkaziyo anatulutsa amunawo powatsitsa ndi chingwe pawindo, pakuti mpanda wa mzindawo unalinso khoma* la nyumba yake, ndipo nyumba yakeyo inali pampandapo.+ Machitidwe 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho usiku, ophunzira ake anamuika m’dengu ndi kumutulutsira pawindo la mpanda, n’kumutsitsira kunja.+ 2 Akorinto 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 koma ndinaikidwa m’dengu n’kutsitsidwa pawindo la mpanda wa mzindawo,+ ndipo ndinapulumuka m’manja mwake.
15 Pambuyo pake, mkaziyo anatulutsa amunawo powatsitsa ndi chingwe pawindo, pakuti mpanda wa mzindawo unalinso khoma* la nyumba yake, ndipo nyumba yakeyo inali pampandapo.+
25 Choncho usiku, ophunzira ake anamuika m’dengu ndi kumutulutsira pawindo la mpanda, n’kumutsitsira kunja.+
33 koma ndinaikidwa m’dengu n’kutsitsidwa pawindo la mpanda wa mzindawo,+ ndipo ndinapulumuka m’manja mwake.