Levitiko 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sabata lililonse azikhazika mkatewo pamaso pa Yehova, ndipo uzikhala pamenepo nthawi zonse.+ Limeneli ndi pangano pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale.
8 Sabata lililonse azikhazika mkatewo pamaso pa Yehova, ndipo uzikhala pamenepo nthawi zonse.+ Limeneli ndi pangano pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale.