-
1 Samueli 26:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Pamene Davide anali kukhala m’chipululu, Sauli anamanga msasa m’mphepete mwa msewu, paphiri la Hakila moyang’anana ndi Yesimoni. Ndiyeno Davide anamva kuti Sauli wabwera kudzam’sakasaka m’chipululumo.
-