Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Akatero anali kupisa mumphika kapena chophikira cha zigwiriro ziwiri, munkhali, kapena m’chophikira cha chigwiriro chimodzi. Ndipo wansembe anali kutenga chilichonse chimene folokoyo yatulutsa. Umu ndi mmene anali kuchitira ku Silo, kwa Aisiraeli onse opita kumeneko.+

  • 1 Samueli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+

  • 1 Samueli 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Eli anali wokalamba kwambiri ndipo anamva+ zonse zimene ana ake anali kuchitira+ Aisiraeli onse, komanso anamva kuti anali kugona ndi akazi+ otumikira pakhomo la chihema chokumanako.+

  • 1 Mafumu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Bambo ake sanafune kumukhumudwitsa pa nthawi ina iliyonse, choncho sanam’dzudzulepo kuti: “Wachitiranji zinthu m’njira imeneyi?”+ Iye analinso wooneka bwino kwambiri,+ ndipo mayi ake anam’bereka pambuyo pobereka Abisalomu.

  • Yakobo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena