1 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamene chaka chinkatha, Hana anatenga pakati ndipo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lake+ Samueli,* chifukwa anati, “ndinam’pempha+ kwa Yehova.” 1 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Samueli anali kutumikira+ pamaso pa Yehova, ali mwana ndipo anali kuvala efodi wansalu.+ 1 Samueli 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+ Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
20 Pamene chaka chinkatha, Hana anatenga pakati ndipo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lake+ Samueli,* chifukwa anati, “ndinam’pempha+ kwa Yehova.”
20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+