Numeri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano khamu lonse la anthuwo litaona kuti Aroni wamwalira, nyumba yonse ya Isiraeli inalira maliro a Aroni masiku 30.+ Deuteronomo 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Isiraeli analira Mose m’chipululu cha Mowabu masiku 30.+ Ndiyeno masiku onse olira maliro a Mose anatha. Machitidwe 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amuna ena oopa Mulungu anatenga Sitefano ndi kukamuika m’manda,+ ndipo anamulira kwambiri.+
29 Tsopano khamu lonse la anthuwo litaona kuti Aroni wamwalira, nyumba yonse ya Isiraeli inalira maliro a Aroni masiku 30.+
8 Ana a Isiraeli analira Mose m’chipululu cha Mowabu masiku 30.+ Ndiyeno masiku onse olira maliro a Mose anatha.