Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 4:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pamenepo mayiyo anapita kwa Elisa n’kugwada pamapazi ake, n’kumuweramira mpaka pansi.+ Kenako ananyamula mwana wakeyo ndipo anatuluka naye.+

  • Esitere 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kuwonjezera pamenepo, Esitere analankhulanso ndi mfumu ndipo anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi pamapazi a mfumuyo. Iye analira+ ndi kuchonderera kuti mfumu imukomere mtima. Ndiponso kuti isinthe choipa+ cha Hamani Mwagagi ndi chiwembu+ chimene anakonzera Ayuda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena