2 Samueli 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo mkazi wa ku Tekowayo anauza mfumu kuti: “Mbuyanga mfumu, kulakwa kukhale kwanga ndi kwa nyumba ya bambo anga,+ koma mfumu ndi mpando wake wachifumu ndi zosalakwa.”
9 Pamenepo mkazi wa ku Tekowayo anauza mfumu kuti: “Mbuyanga mfumu, kulakwa kukhale kwanga ndi kwa nyumba ya bambo anga,+ koma mfumu ndi mpando wake wachifumu ndi zosalakwa.”