1 Samueli 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero iwo ananyamuka ndi kupita ku Zifi,+ Sauli atamusiya kumbuyo. Izi zinachitika pamene Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali m’chipululu cha Maoni,+ mu Araba,+ kum’mwera kwa Yesimoni.
24 Chotero iwo ananyamuka ndi kupita ku Zifi,+ Sauli atamusiya kumbuyo. Izi zinachitika pamene Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali m’chipululu cha Maoni,+ mu Araba,+ kum’mwera kwa Yesimoni.