Levitiko 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.