1 Mafumu 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+ 1 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.
35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+
22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.