Salimo 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Masautso a mtima wanga awonjezeka.+Ndilanditseni ku nkhawa zimene zili pa ine.+ Salimo 116:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+
3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+