Genesis 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Rakele ataona kuti sanaberekere Yakobo mwana, anayamba kuchitira nsanje m’bale wake. Iye anauza Yakobo+ kuti: “Mundipatse ana, apo ayi kuli bwino ndingofa.”+
30 Ndiyeno Rakele ataona kuti sanaberekere Yakobo mwana, anayamba kuchitira nsanje m’bale wake. Iye anauza Yakobo+ kuti: “Mundipatse ana, apo ayi kuli bwino ndingofa.”+