Levitiko 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Numeri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Zopereka zonse+ za zinthu zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+
3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.
9 “‘Zopereka zonse+ za zinthu zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+