1 Samueli 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mukachita zinthu zoipa mouma khosi, mudzasesedwa,+ inu pamodzi ndi mfumu yanuyo.”+ 1 Mbiri 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Afilisiti+ anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo amuna a Isiraeli anali kuthawa pamaso pa Afilisitiwo, moti anali kuphedwa m’phiri la Giliboa.+
10 Tsopano Afilisiti+ anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo amuna a Isiraeli anali kuthawa pamaso pa Afilisitiwo, moti anali kuphedwa m’phiri la Giliboa.+