Ezekieli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Posachedwapa, ndikukhuthulirani ukali wanga,+ ndipo mkwiyo wanga ndiuthetsera pa inu.+ Ndikuweruzani mogwirizana ndi njira zanu,+ ndipo ndikubwezerani chifukwa cha zonyansa zanu zonse. Ezekieli 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+
8 “‘Posachedwapa, ndikukhuthulirani ukali wanga,+ ndipo mkwiyo wanga ndiuthetsera pa inu.+ Ndikuweruzani mogwirizana ndi njira zanu,+ ndipo ndikubwezerani chifukwa cha zonyansa zanu zonse.
30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+