1 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa. 1 Samueli 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+
16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa.
14 Kenako Samueli anauza anthuwo kuti: “Tiyeni tipite ku Giligala+ kuti tikachitenso mwambo wolonga mfumu.”+