1 Samueli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Samueli anapitiriza kukula ndipo Yehova anali naye,+ moti palibe mawu ake alionse amene anapita padera.+ Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
19 Samueli anapitiriza kukula ndipo Yehova anali naye,+ moti palibe mawu ake alionse amene anapita padera.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+