1 Samueli 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake analumbirira anthu.+ Chotero anatambasula dzanja lake ndi kukhudza chisa cha uchi ndi ndodo. Kenako ananyambita ndodoyo, ndipo atatero, anayera m’maso.+
27 Koma Yonatani sanamve pamene bambo ake analumbirira anthu.+ Chotero anatambasula dzanja lake ndi kukhudza chisa cha uchi ndi ndodo. Kenako ananyambita ndodoyo, ndipo atatero, anayera m’maso.+