Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Zekariya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+