1 Mafumu 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Ahiya anatenga chovala chatsopano chimene anavala chija n’kuching’ambang’amba+ zidutswa zokwana 12.+
30 Ndiyeno Ahiya anatenga chovala chatsopano chimene anavala chija n’kuching’ambang’amba+ zidutswa zokwana 12.+