Yobu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi maso anu+ ali ngati a munthu,Kapena kodi mumaona ngati mmene munthu amaonera?+ Yesaya 55:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Maganizo a anthu inu si maganizo anga,+ ndipo njira zanga si njira zanu,”+ akutero Yehova.