1 Samueli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zitatero, Sauli anachita mantha+ ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atam’chokera.+
12 Zitatero, Sauli anachita mantha+ ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atam’chokera.+