1 Samueli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anali kupita kwa Sauli ndi kubwerera ku Betelehemu kukaweta nkhosa+ za bambo ake. Salimo 78:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Choncho anasankha Davide mtumiki wake,+Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa.+